Penapake tizikhala serious, munthu sungamadisane ndi munthu woti u know zoti Ali wack kale (zili ngati kukwapulila mwana ndi chikwanje Malo mwa chikwapu). Ngti mukuzithemba Wu hiphop, diss wth ur fellow heavyweight.
Komanso kumenya chizungu chazi mawu zikuluzikulu si Wu lyricist